Amangidwa atapezeka ndi Chamba.
Wolemba William Chitengu Jnr A Polisi m’boma la Salima amanga abambo atatu kamba kopezeka ndi chamba opanda chilorezo. Malingana ndi Mneneri wa…
Wolemba William Chitengu Jnr A Polisi m’boma la Salima amanga abambo atatu kamba kopezeka ndi chamba opanda chilorezo. Malingana ndi Mneneri wa…
Picture: Sub Inspector Rabecca Ndiwate By Stella Chasowa A 52 year old driver named Robert Gabiseni has died, while three others have…
Atengambali pa Mkumanowu. Wolemba William Chitengu Jnr Bungwe loyendetsa komanso kuyang’anira masewero a mulosera mdziko muno la Malawi Gaming and Lotteries Authority…
Chithunzi: James Manyetera A James Manyetera omwe amafuna kupikisana nawo pa zisankho za Chipulula za Chipani cha Malawi Congress (MCP) ati asintha…
Wolemba William Chitengu Unduna owona za chilengedwe ndikusintha kwa nyengo kudzera ku nthambi yoona za nkhalango, walengeza kutseka kwa nyengo yodzala mitengo…
Wolemba Stella Chasowa Pali chiyembekezo chakuti ophunzira pa sukulu ya Chagunda akhala ndi zipinda zophunzirira zabwino pomwe phungu wanyumba yamalamulo wa derali…
Senior Group Sosola Bungwe la Malawi Chewa Heritage (MACHE) lachenjeza mafumu kuti asachite mchitidwe wolanda ndalama kwa anthu ogula mbewu pofuna kuti…
Chithunzi Adams Cuba Phiri. Wolemba Liana Bonongwe Adams Curba Phiri ndiye wapambana pa udindo wa wapampando wa Salima district football association (SADFA)…
Lumbani Mgula Wolemba Chisomo Mpaso. Pamene zisankho zapatatu zikuyandikila mmwezi wa September pa 16, Bungwe la Umunthu Plus laphunzitsa gulu la amayi…
Wolemba Liana Bonongwe Bungwe la world vision Malawi lapeleka ufa wa phala wa likuni wandalama zokwana 28 million kwacha ku sukulu ya…