Apempha boma kuwathandiza ndi misika.
Alimi omwe amachita Ulimi wa mthilira ochokera m’mudzi mwa Group Village Mtende Mfumu yaikulu Pemba m’boma la Salima apempha boma kuti liwathandize…
Alimi omwe amachita Ulimi wa mthilira ochokera m’mudzi mwa Group Village Mtende Mfumu yaikulu Pemba m’boma la Salima apempha boma kuti liwathandize…
Wolemba Chisomo Mpaso Katswiri pa nkhani zamalimidwe Leonard Chimwaza wapempha alimi m’dziko muno kuti aonetsetse kuti mitengo yogulira mbewu yomwe yangotulutsidwa kumene…